1 Atesalonika 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chifukwa inu abale munatsanzira mipingo ya Mulungu yogwirizana ndi Khristu Yesu imene ili ku Yudeya. Tikutero chifukwa munayamba kuvutitsidwa ndi anthu akwanu,+ ngati mmene iwowonso akuvutitsidwira ndi Ayuda.
14 Chifukwa inu abale munatsanzira mipingo ya Mulungu yogwirizana ndi Khristu Yesu imene ili ku Yudeya. Tikutero chifukwa munayamba kuvutitsidwa ndi anthu akwanu,+ ngati mmene iwowonso akuvutitsidwira ndi Ayuda.