Akolose 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tachita zimenezi nʼcholinga choti mukhale ndi khalidwe logwirizana* ndi zimene Yehova* amafuna, kuti muzimusangalatsa pa chilichonse, pamene mukupitiriza kubala zipatso pantchito iliyonse yabwino ndi kuwonjezera kumudziwa Mulungu molondola.+ 1 Petulo 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mukhale ndi khalidwe labwino pakati pa anthu amʼdzikoli,+ kuti akamakunenani kuti mumachita zoipa, aziona okha zochita zanu zabwino+ kuti kenako adzatamande Mulungu patsiku lake loyendera.
10 Tachita zimenezi nʼcholinga choti mukhale ndi khalidwe logwirizana* ndi zimene Yehova* amafuna, kuti muzimusangalatsa pa chilichonse, pamene mukupitiriza kubala zipatso pantchito iliyonse yabwino ndi kuwonjezera kumudziwa Mulungu molondola.+
12 Mukhale ndi khalidwe labwino pakati pa anthu amʼdzikoli,+ kuti akamakunenani kuti mumachita zoipa, aziona okha zochita zanu zabwino+ kuti kenako adzatamande Mulungu patsiku lake loyendera.