Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 79:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Tsanulirani mkwiyo wanu pa mitundu ya anthu amene sakukudziwani

      Komanso pa maufumu amene saitana pa dzina lanu.+

  • Aefeso 4:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Choncho ndikunena komanso kuchitira umboni mwa Ambuye, kuti musapitirize kuyenda ngati mmene anthu a mitundu ina amayendera,+ potsatira maganizo awo opanda pake.+

  • Aefeso 4:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Popeza iwo sakuthanso kuzindikira makhalidwe abwino, anadzipereka okha ku khalidwe lopanda manyazi*+ kuti achite zonyansa zamtundu uliwonse mwadyera.

  • 1 Petulo 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mʼmbuyomu munkangokhalira kuchita zofuna za anthu amʼdzikoli.+ Pa nthawi imeneyo munkachita khalidwe lopanda manyazi,* munkalakalaka zoipa, munkamwa vinyo mopitirira muyezo, munkakonda maphwando oipa,* munkapanga mipikisano yomwa mowa komanso munkapembedza mafano, komwe kunali kuphwanya malamulo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena