18 Thawani chiwerewere.*+ Tchimo lililonse limene munthu angachite ndi la kunja kwa thupi lake, koma amene amachita chiwerewere amachimwira thupi lake.+
5 Chifukwa mfundo iyi mukuidziwa ndipo mukuimvetsa bwino, kuti munthu wachiwerewere*+ kapena wodetsedwa kapena waumbombo,+ umene ndi kulambira mafano, sadzalowa mu Ufumu wa Khristu ndi wa Mulungu.+