Aheberi 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Muziyesetsa kukhala mwamtendere ndi anthu onse,+ komanso kukhala oyera+ chifukwa ngati munthu si woyera, sadzaona Ambuye. 1 Petulo 1:15, 16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma mofanana ndi Woyera amene anakuitanani, inunso khalani oyera mʼmakhalidwe anu onse,+ 16 chifukwa Malemba amati: “Mukhale oyera, chifukwa ine ndine woyera.”+
14 Muziyesetsa kukhala mwamtendere ndi anthu onse,+ komanso kukhala oyera+ chifukwa ngati munthu si woyera, sadzaona Ambuye.
15 Koma mofanana ndi Woyera amene anakuitanani, inunso khalani oyera mʼmakhalidwe anu onse,+ 16 chifukwa Malemba amati: “Mukhale oyera, chifukwa ine ndine woyera.”+