-
1 Akorinto 6:18, 19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Thawani chiwerewere.*+ Tchimo lililonse limene munthu angachite ndi la kunja kwa thupi lake, koma amene amachita chiwerewere amachimwira thupi lake.+ 19 Kodi inu simukudziwa kuti thupi lanu ndi kachisi+ wa mzimu woyera umene uli mwa inu, womwe munapatsidwa ndi Mulungu?+ Ndiponso mwiniwake wa inuyo si inu,+
-