1 Yohane 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Komanso, munthu womvera malamulo ake amakhalabe wogwirizana naye ndipo iyenso amakhala wogwirizana ndi munthuyo.+ Ndiponso chifukwa cha mzimu umene anatipatsa, timadziwa kuti ndife ogwirizana naye.+
24 Komanso, munthu womvera malamulo ake amakhalabe wogwirizana naye ndipo iyenso amakhala wogwirizana ndi munthuyo.+ Ndiponso chifukwa cha mzimu umene anatipatsa, timadziwa kuti ndife ogwirizana naye.+