Yohane 13:34, 35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndikukupatsani lamulo latsopano, kuti muzikondana. Mofanana ndi mmene ine ndakukonderani,+ inunso muzikondana choncho.+ 35 Onse adzadziwa kuti ndinu ophunzira anga ngati mukukondana.”+ 1 Petulo 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Popeza mwadziyeretsa pokhala omvera choonadi cha mʼMawu a Mulungu ndipo tsopano mumakonda abale mopanda chinyengo,+ muzikondana kwambiri kuchokera mumtima.+ 1 Yohane 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo iye anatipatsa lamulo lakuti, munthu amene amakonda Mulungu azikondanso mʼbale wake.+
34 Ndikukupatsani lamulo latsopano, kuti muzikondana. Mofanana ndi mmene ine ndakukonderani,+ inunso muzikondana choncho.+ 35 Onse adzadziwa kuti ndinu ophunzira anga ngati mukukondana.”+
22 Popeza mwadziyeretsa pokhala omvera choonadi cha mʼMawu a Mulungu ndipo tsopano mumakonda abale mopanda chinyengo,+ muzikondana kwambiri kuchokera mumtima.+