Maliko 9:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Mchere ndi wabwino, koma ngati mcherewo watha mphamvu, kodi mphamvuyo mungaibwezeretse bwanji?+ Khalani ndi mchere mwa inu nokha+ ndipo sungani mtendere pakati panu.”+ 2 Akorinto 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pomaliza abale, pitirizani kusangalala, kusintha maganizo, kulimbikitsidwa,+ kukhala ndi maganizo ogwirizana+ ndiponso kukhala mwamtendere.+ Mukatero, Mulungu amene ndi wachikondi komanso wamtendere+ adzakhala nanu.
50 Mchere ndi wabwino, koma ngati mcherewo watha mphamvu, kodi mphamvuyo mungaibwezeretse bwanji?+ Khalani ndi mchere mwa inu nokha+ ndipo sungani mtendere pakati panu.”+
11 Pomaliza abale, pitirizani kusangalala, kusintha maganizo, kulimbikitsidwa,+ kukhala ndi maganizo ogwirizana+ ndiponso kukhala mwamtendere.+ Mukatero, Mulungu amene ndi wachikondi komanso wamtendere+ adzakhala nanu.