-
Yobu 2:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ndiyeno Yehova anafunsanso Satana kuti: “Kodi mtima wako uli pa mtumiki wanga Yobu? Padziko lapansi palibe wina wofanana naye. Iye ndi munthu wokhulupirika amene amachita zoyenera,*+ amaopa Mulungu ndiponso amapewa zoipa. Iye akupitirizabe kukhala wokhulupirika+ ngakhale kuti iweyo ukufuna kuti ndimuwononge*+ popanda chifukwa.”
-