Mateyu 24:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chifukwa kudzabwera anthu onamizira kuti ndi Khristu komanso aneneri abodza+ ndipo adzachita zizindikiro zamphamvu ndiponso zodabwitsa, kuti ngati nʼkotheka, adzasocheretse+ ngakhale osankhidwawo.
24 Chifukwa kudzabwera anthu onamizira kuti ndi Khristu komanso aneneri abodza+ ndipo adzachita zizindikiro zamphamvu ndiponso zodabwitsa, kuti ngati nʼkotheka, adzasocheretse+ ngakhale osankhidwawo.