Machitidwe 19:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho mawu a Yehova* anapitiriza kufalikira ndipo sankagonjetseka.+ 1 Atesalonika 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Sikuti mawu a Yehova* ochokera kwa inu amveka ku Makedoniya ndi ku Akaya kokha, koma kwina kulikonse chikhulupiriro chanu mwa Mulungu chafalikira,+ moti ife sitikufunika kunenapo kanthu.
8 Sikuti mawu a Yehova* ochokera kwa inu amveka ku Makedoniya ndi ku Akaya kokha, koma kwina kulikonse chikhulupiriro chanu mwa Mulungu chafalikira,+ moti ife sitikufunika kunenapo kanthu.