2 Petulo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma ndi mawu a Mulungu omwewo, kumwamba ndi dziko lapansi zimene zilipo panopa, azisungira moto ndipo akuzisungabe mpaka pa tsiku limene adzaweruze komanso kuwononga anthu osaopa Mulungu.+
7 Koma ndi mawu a Mulungu omwewo, kumwamba ndi dziko lapansi zimene zilipo panopa, azisungira moto ndipo akuzisungabe mpaka pa tsiku limene adzaweruze komanso kuwononga anthu osaopa Mulungu.+