-
1 Akorinto 15:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Yambani kuganiza mwanzeru nʼkumachita zoyenera ndipo musamachite tchimo. Ena a inu sadziwa Mulungu. Ndikulankhula zimenezi kuti ndikuchititseni manyazi.
-