2 Timoteyo 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Uziwakumbutsa zimenezi nthawi zonse. Uziwalangiza* pamaso pa Mulungu, kuti asamakangane pa mawu. Kuchita zimenezi kulibe phindu mʼpangʼono pomwe chifukwa kumawononga chikhulupiriro cha omvetsera. Tito 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa pali anthu ambiri osalamulirika, olankhula zosathandiza ndiponso opusitsa ena, ndipo pakati pa anthu amenewa palinso amene akulimbikitsabe mdulidwe.+ Tito 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma iwe uzipewa kutsutsana pa zinthu zopusa komanso zokhudza mibadwo ya makolo. Uzipewanso kukangana ndi kulimbana ndi anthu pa nkhani zokhudza Chilamulo, chifukwa zimenezi nʼzosathandiza ndiponso zopanda phindu.+
14 Uziwakumbutsa zimenezi nthawi zonse. Uziwalangiza* pamaso pa Mulungu, kuti asamakangane pa mawu. Kuchita zimenezi kulibe phindu mʼpangʼono pomwe chifukwa kumawononga chikhulupiriro cha omvetsera.
10 Chifukwa pali anthu ambiri osalamulirika, olankhula zosathandiza ndiponso opusitsa ena, ndipo pakati pa anthu amenewa palinso amene akulimbikitsabe mdulidwe.+
9 Koma iwe uzipewa kutsutsana pa zinthu zopusa komanso zokhudza mibadwo ya makolo. Uzipewanso kukangana ndi kulimbana ndi anthu pa nkhani zokhudza Chilamulo, chifukwa zimenezi nʼzosathandiza ndiponso zopanda phindu.+