1 Timoteyo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chifukwa kuchita masewera olimbitsa thupi ndi kothandiza pangʼono, koma kukhala wodzipereka kwa Mulungu ndi kothandiza pa zinthu zonse, chifukwa kumakhudza lonjezo la moyo wathu panopa ndi moyo umene ukubwerawo.+
8 Chifukwa kuchita masewera olimbitsa thupi ndi kothandiza pangʼono, koma kukhala wodzipereka kwa Mulungu ndi kothandiza pa zinthu zonse, chifukwa kumakhudza lonjezo la moyo wathu panopa ndi moyo umene ukubwerawo.+