Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Luka 5:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Ine sindinabwere kudzaitana anthu olungama, koma ochimwa kuti alape.”+

  • 2 Akorinto 5:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Utumiki wake ndi woti tilengeze kuti Mulungu ankagwirizanitsa dziko ndi iyeyo kudzera mwa Khristu,+ moti sanawawerengere anthuwo zolakwa zawo,+ ndipo watipatsa ifeyo ntchito yolalikira uthenga wothandiza anthu kugwirizananso ndi Mulungu.+

  • 1 Yohane 2:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ana anga okondedwa, ndikukulemberani zinthu izi kuti musachite tchimo. Komabe, wina akachita tchimo, tili ndi wotithandiza wolungama,+ Yesu Khristu,+ amene ali ndi Atate. 2 Iye anakhala nsembe yophimba+ machimo athu.*+ Osati athu okha, komanso a dziko lonse lapansi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena