Genesis 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Yehova Mulungu anati: “Si bwino kuti munthu azikhala yekha. Ndimupangira womuthandiza, monga mnzake womuyenerera.”+ Genesis 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno Yehova Mulungu anapanga mkazi kuchokera kunthiti imene anaichotsa kwa mwamunayo. Atatero, anamupititsa kwa iye.+ 1 Akorinto 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chifukwa mwamuna sanachokere kwa mkazi, koma mkazi anachokera kwa mwamuna.+
18 Kenako Yehova Mulungu anati: “Si bwino kuti munthu azikhala yekha. Ndimupangira womuthandiza, monga mnzake womuyenerera.”+
22 Ndiyeno Yehova Mulungu anapanga mkazi kuchokera kunthiti imene anaichotsa kwa mwamunayo. Atatero, anamupititsa kwa iye.+