-
Yohane 13:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Atatero anathira madzi mʼbeseni nʼkuyamba kusambitsa mapazi a ophunzirawo komanso kuwapukuta ndi thaulo limene anamanga mʼchiuno lija.
-