1 Timoteyo 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ukamapereka malangizowa kwa abale, udzakhala mtumiki wabwino wa Khristu Yesu. Ndipo udzakula bwino ndi mawu a chikhulupiriro ndiponso chiphunzitso chabwino chimene wachitsatira mosamala.+
6 Ukamapereka malangizowa kwa abale, udzakhala mtumiki wabwino wa Khristu Yesu. Ndipo udzakula bwino ndi mawu a chikhulupiriro ndiponso chiphunzitso chabwino chimene wachitsatira mosamala.+