Mateyu 10:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma aliyense amene adzandikane pamaso pa anthu, inenso ndidzamukana pamaso pa Atate wanga wakumwamba.+ Luka 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma aliyense amene adzandikane pamaso pa anthu, adzakanidwa pamaso pa angelo a Mulungu.+
33 Koma aliyense amene adzandikane pamaso pa anthu, inenso ndidzamukana pamaso pa Atate wanga wakumwamba.+