Akolose 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano ndikusangalala ndi mavuto amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu.+ Ndipo inenso ndikuona kuti sindinazunzikebe mokwanira monga chiwalo cha thupi la Khristu,+ limene ndi mpingo.+ 2 Timoteyo 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Monga msilikali wabwino+ wa Khristu Yesu, khala wokonzeka kukumana ndi mavuto.+
24 Tsopano ndikusangalala ndi mavuto amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu.+ Ndipo inenso ndikuona kuti sindinazunzikebe mokwanira monga chiwalo cha thupi la Khristu,+ limene ndi mpingo.+