Mateyu 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mofanana ndi zimenezi, nanunso muzionetsa kuwala kwanu pamaso pa anthu,+ kuti aone ntchito zanu zabwino+ nʼkulemekeza Atate wanu wakumwamba.+
16 Mofanana ndi zimenezi, nanunso muzionetsa kuwala kwanu pamaso pa anthu,+ kuti aone ntchito zanu zabwino+ nʼkulemekeza Atate wanu wakumwamba.+