1 Yohane 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chifukwa chilichonse chamʼdzikoli, monga zimene thupi limalakalaka,+ zimene maso amalakalaka+ komanso kudzionetsera ndi zinthu zimene munthu ali nazo pa moyo wake,* sizichokera kwa Atate koma mʼdzikoli.
16 Chifukwa chilichonse chamʼdzikoli, monga zimene thupi limalakalaka,+ zimene maso amalakalaka+ komanso kudzionetsera ndi zinthu zimene munthu ali nazo pa moyo wake,* sizichokera kwa Atate koma mʼdzikoli.