Aroma 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho, mmene zinakhalira kuti uchimo umodzi unachititsa kuti anthu osiyanasiyana aweruzidwe kuti ndi ochimwa,+ kuchita chinthu chimodzi cholungama kwachititsanso kuti anthu osiyanasiyana+ aonedwe kuti ndi olungama kuti akhale ndi moyo.+
18 Choncho, mmene zinakhalira kuti uchimo umodzi unachititsa kuti anthu osiyanasiyana aweruzidwe kuti ndi ochimwa,+ kuchita chinthu chimodzi cholungama kwachititsanso kuti anthu osiyanasiyana+ aonedwe kuti ndi olungama kuti akhale ndi moyo.+