Aheberi 7:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Chilamulo chimaika amuna okhala ndi zofooka kukhala akulu a ansembe.+ Koma mawu a lumbiro+ amene ananenedwa pambuyo pa Chilamulo anaika Mwana, amene anakhala wangwiro+ mpaka kalekale.
28 Chilamulo chimaika amuna okhala ndi zofooka kukhala akulu a ansembe.+ Koma mawu a lumbiro+ amene ananenedwa pambuyo pa Chilamulo anaika Mwana, amene anakhala wangwiro+ mpaka kalekale.