Aheberi 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho, abale athu oyera, amene muli mʼgulu la anthu oitanidwa kumwamba,+ ganizirani za Yesu, mtumwi ndi mkulu wa ansembe amene tikumuvomereza.+ Aheberi 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mkulu wa ansembe ngati ameneyu ndi wotiyeneradi chifukwa ndi wokhulupirika, wosalakwa, wosaipitsidwa,+ wosiyana ndi anthu ochimwa ndipo wakwezedwa pamwamba kwambiri.+
3 Choncho, abale athu oyera, amene muli mʼgulu la anthu oitanidwa kumwamba,+ ganizirani za Yesu, mtumwi ndi mkulu wa ansembe amene tikumuvomereza.+
26 Mkulu wa ansembe ngati ameneyu ndi wotiyeneradi chifukwa ndi wokhulupirika, wosalakwa, wosaipitsidwa,+ wosiyana ndi anthu ochimwa ndipo wakwezedwa pamwamba kwambiri.+