-
Levitiko 9:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Ndiyeno anaperekera nsembe anthu. Anatenga mbuzi yoperekera anthu nsembe yamachimo ndipo anaipha, nʼkuipereka monga nsembe yamachimo, mmene anachitira ndi nyama yoyamba ija.
-