Aheberi 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho mzimu woyera umatithandiza kumvetsa bwino kuti njira yolowera kumalo oyera inali isanaonekere pamene chihema choyambacho chinalipo.+ Aheberi 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Khristu sanalowe mʼmalo oyera opangidwa ndi manja a anthu,+ amene ndi chithunzi cha malo enieniwo,+ koma analowa kumwamba kwenikweniko.+ Panopa iye ali kumwamba kuti azionekera pamaso pa Mulungu mʼmalo mwa ifeyo.+
8 Choncho mzimu woyera umatithandiza kumvetsa bwino kuti njira yolowera kumalo oyera inali isanaonekere pamene chihema choyambacho chinalipo.+
24 Khristu sanalowe mʼmalo oyera opangidwa ndi manja a anthu,+ amene ndi chithunzi cha malo enieniwo,+ koma analowa kumwamba kwenikweniko.+ Panopa iye ali kumwamba kuti azionekera pamaso pa Mulungu mʼmalo mwa ifeyo.+