Aefeso 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ndipo pitirizani kusonyeza chikondi+ ngati mmene Khristu anatikondera*+ nʼkudzipereka yekha chifukwa cha ife* ngati chopereka ndiponso ngati nsembe yafungo lokoma kwa Mulungu.+
2 ndipo pitirizani kusonyeza chikondi+ ngati mmene Khristu anatikondera*+ nʼkudzipereka yekha chifukwa cha ife* ngati chopereka ndiponso ngati nsembe yafungo lokoma kwa Mulungu.+