Ekisodo 36:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kenako anapanga katani+ ya ulusi wabuluu, ya ubweya wa nkhosa wapepo, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota wabwino kwambiri. Pakataniyo anapetapo+ akerubi.+
35 Kenako anapanga katani+ ya ulusi wabuluu, ya ubweya wa nkhosa wapepo, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota wabwino kwambiri. Pakataniyo anapetapo+ akerubi.+