Ekisodo 16:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndiyeno Mose anauza Aroni kuti: “Tenga mtsuko ndipo uthiremo mana okwana muyezo umodzi wa omeri nʼkuuika pamaso pa Yehova kuti asungidwe mʼmibadwo yanu yonse.”+
33 Ndiyeno Mose anauza Aroni kuti: “Tenga mtsuko ndipo uthiremo mana okwana muyezo umodzi wa omeri nʼkuuika pamaso pa Yehova kuti asungidwe mʼmibadwo yanu yonse.”+