Aheberi 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kulinso Yesu, mkhalapakati+ wa pangano latsopano,+ ndiponso magazi amene awazidwa, omwe amalankhula mʼnjira yabwino kwambiri kuposa magazi a Abele.+ Aheberi 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano, Mulungu wamtendere amene anaukitsa mʼbusa wamkulu+ wa nkhosa amene ali ndi magazi a pangano losatha, Ambuye wathu Yesu,
24 Kulinso Yesu, mkhalapakati+ wa pangano latsopano,+ ndiponso magazi amene awazidwa, omwe amalankhula mʼnjira yabwino kwambiri kuposa magazi a Abele.+
20 Tsopano, Mulungu wamtendere amene anaukitsa mʼbusa wamkulu+ wa nkhosa amene ali ndi magazi a pangano losatha, Ambuye wathu Yesu,