Zekariya 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munthu ameneyu ndi amene adzamange kachisi wa Yehova ndipo adzalandira ulemerero. Iye adzakhala pampando wake wachifumu nʼkumalamulira. Adzakhalanso wansembe ali pampando womwewo+ ndipo maudindo awiri onsewo adzakhala ogwirizana. Aheberi 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma Khristu anali mwana ndipo ankayangʼanira nyumba ya Mulungu mokhulupirika.+ Ife tikhalabe nyumba ya Mulunguyo+ tikapitiriza kukhala ndi ufulu wa kulankhula komanso kugwira mwamphamvu chiyembekezo chimene timachinyadira mpaka mapeto.
13 Munthu ameneyu ndi amene adzamange kachisi wa Yehova ndipo adzalandira ulemerero. Iye adzakhala pampando wake wachifumu nʼkumalamulira. Adzakhalanso wansembe ali pampando womwewo+ ndipo maudindo awiri onsewo adzakhala ogwirizana.
6 Koma Khristu anali mwana ndipo ankayangʼanira nyumba ya Mulungu mokhulupirika.+ Ife tikhalabe nyumba ya Mulunguyo+ tikapitiriza kukhala ndi ufulu wa kulankhula komanso kugwira mwamphamvu chiyembekezo chimene timachinyadira mpaka mapeto.