Akolose 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chilichonse chimene mukuchita, muzichichita ndi moyo wanu wonse ngati kuti mukuchitira Yehova,*+ osati anthu, 1 Timoteyo 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Uwauze kuti azichita zabwino, akhale olemera pa ntchito zabwino, owolowa manja komanso okonzeka kugawira ena+
23 Chilichonse chimene mukuchita, muzichichita ndi moyo wanu wonse ngati kuti mukuchitira Yehova,*+ osati anthu,
18 Uwauze kuti azichita zabwino, akhale olemera pa ntchito zabwino, owolowa manja komanso okonzeka kugawira ena+