2 Petulo 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Zikanakhala bwino akanapanda kudziwa molondola njira ya chilungamo, kusiyana nʼkuidziwa bwinobwino kenako nʼkupatuka pa malamulo oyera omwe analandira.+
21 Zikanakhala bwino akanapanda kudziwa molondola njira ya chilungamo, kusiyana nʼkuidziwa bwinobwino kenako nʼkupatuka pa malamulo oyera omwe analandira.+