Deuteronomo 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Munthuyo aziphedwa ngati pali umboni wa* anthu awiri kapena atatu.+ Asaphedwe ngati munthu mmodzi yekha ndi amene wapereka umboni.+
6 Munthuyo aziphedwa ngati pali umboni wa* anthu awiri kapena atatu.+ Asaphedwe ngati munthu mmodzi yekha ndi amene wapereka umboni.+