Mateyu 26:27, 28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako anatenga kapu ya vinyo ndipo atayamika, anaipereka kwa iwo nʼkunena kuti: “Imwani nonsenu.+ 28 Vinyoyu akuimira ‘magazi anga+ a pangano,’+ amene adzakhetsedwe chifukwa cha anthu ambiri+ kuti machimo awo akhululukidwe.+ Luka 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Anachitanso chimodzimodzi ndi kapu atadya chakudya chamadzulocho. Iye anati: “Kapu iyi ikuimira pangano latsopano+ limene linakhazikitsidwa pogwiritsa ntchito magazi anga,+ amene adzakhetsedwe chifukwa cha inu.+
27 Kenako anatenga kapu ya vinyo ndipo atayamika, anaipereka kwa iwo nʼkunena kuti: “Imwani nonsenu.+ 28 Vinyoyu akuimira ‘magazi anga+ a pangano,’+ amene adzakhetsedwe chifukwa cha anthu ambiri+ kuti machimo awo akhululukidwe.+
20 Anachitanso chimodzimodzi ndi kapu atadya chakudya chamadzulocho. Iye anati: “Kapu iyi ikuimira pangano latsopano+ limene linakhazikitsidwa pogwiritsa ntchito magazi anga,+ amene adzakhetsedwe chifukwa cha inu.+