Mateyu 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Sangalalani ndi kukondwera+ kwambiri chifukwa mphoto+ imene Mulungu adzakupatseni ndi yaikulu,* ndipo umu ndi mmenenso anazunzira aneneri amene analipo inu musanakhaleko.+
12 Sangalalani ndi kukondwera+ kwambiri chifukwa mphoto+ imene Mulungu adzakupatseni ndi yaikulu,* ndipo umu ndi mmenenso anazunzira aneneri amene analipo inu musanakhaleko.+