Habakuku 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa masomphenyawa akudikira nthawi yake yoikidwiratu,Atsala pangʼono kukwaniritsidwa* ndipo zimene zili mʼmasomphenyawa si zonama. Ngakhale atachedwa* uziwayembekezerabe,*+ Chifukwa adzakwaniritsidwa ndithu. Sadzachedwa. 2 Petulo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova* sakuchedwa kukwaniritsa zimene analonjeza+ ngati mmene anthu ena amaonera kuti akuchedwa. Koma akukulezerani mtima chifukwa sakufuna kuti munthu aliyense adzawonongedwe, koma akufuna kuti anthu onse alape.+
3 Chifukwa masomphenyawa akudikira nthawi yake yoikidwiratu,Atsala pangʼono kukwaniritsidwa* ndipo zimene zili mʼmasomphenyawa si zonama. Ngakhale atachedwa* uziwayembekezerabe,*+ Chifukwa adzakwaniritsidwa ndithu. Sadzachedwa.
9 Yehova* sakuchedwa kukwaniritsa zimene analonjeza+ ngati mmene anthu ena amaonera kuti akuchedwa. Koma akukulezerani mtima chifukwa sakufuna kuti munthu aliyense adzawonongedwe, koma akufuna kuti anthu onse alape.+