Habakuku 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Taona munthu wodzikuza,Mtima wake si wowongoka. Koma wolungama adzakhala ndi moyo chifukwa cha kukhulupirika kwake.*+
4 Taona munthu wodzikuza,Mtima wake si wowongoka. Koma wolungama adzakhala ndi moyo chifukwa cha kukhulupirika kwake.*+