Genesis 6:8, 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Yehova ankasangalala ndi Nowa. 9 Iyi ndi mbiri ya Nowa. Nowa anali munthu wolungama.+ Iye anali wopanda cholakwa pakati pa anthu a mʼnthawi yake. Nowa anayenda ndi Mulungu woona.+
8 Koma Yehova ankasangalala ndi Nowa. 9 Iyi ndi mbiri ya Nowa. Nowa anali munthu wolungama.+ Iye anali wopanda cholakwa pakati pa anthu a mʼnthawi yake. Nowa anayenda ndi Mulungu woona.+