Genesis 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo Nowa anachita zonse mogwirizana ndi zimene Mulungu anamulamula. Anachitadi zomwezo.+ 2 Petulo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mulungu sanalekerere dziko lakale lija osalipatsa chilango,+ koma anasunga Nowa, yemwe ankalalikira za chilungamo cha Mulungu.+ Anamupulumutsa limodzi ndi anthu enanso 7,+ pamene anabweretsa chigumula padziko la anthu osaopa Mulungu.+
5 Mulungu sanalekerere dziko lakale lija osalipatsa chilango,+ koma anasunga Nowa, yemwe ankalalikira za chilungamo cha Mulungu.+ Anamupulumutsa limodzi ndi anthu enanso 7,+ pamene anabweretsa chigumula padziko la anthu osaopa Mulungu.+