Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 4:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndiye kodi anthu odulidwa okha ndi amene amakhala osangalala choncho? Kapena osadulidwa nawonso amakhala osangalala?+ Popeza timati: “Abulahamu anaonedwa kuti ndi wolungama chifukwa cha chikhulupiriro chake.”+

  • Aroma 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndipo Mulungu anapatsa Abulahamu mdulidwe ngati chizindikiro+ chosonyeza kuti Mulungu anamuona kuti ndi wolungama asanadulidwe chifukwa cha chikhulupiriro. Anachita zimenezi kuti adzakhale bambo wa onse osadulidwa amene ali ndi chikhulupiriro,+ kuti anthuwo adzaonedwe kuti ndi olungama.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena