Yohane 8:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Atate wanu Abulahamu ankasangalala kwambiri chifukwa ankayembekezera kuona tsiku langa, moti analionadi ndipo anasangalala.”+
56 Atate wanu Abulahamu ankasangalala kwambiri chifukwa ankayembekezera kuona tsiku langa, moti analionadi ndipo anasangalala.”+