Genesis 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako Mulungu anauza Abulahamu kuti: “Usaipidwe ndi zimene Sara akukuuza zokhudza mnyamatayo ndiponso kapolo wakoyo. Mumvere,* chifukwa mbadwa* zimene ndinakulonjeza zidzachokera mwa Isaki.+
12 Kenako Mulungu anauza Abulahamu kuti: “Usaipidwe ndi zimene Sara akukuuza zokhudza mnyamatayo ndiponso kapolo wakoyo. Mumvere,* chifukwa mbadwa* zimene ndinakulonjeza zidzachokera mwa Isaki.+