-
Genesis 48:15, 16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Kenako anadalitsa Yosefe kuti:+
“Mulungu woona amene makolo anga Abulahamu ndi Isaki anayenda pamaso pake,+
Mulungu woona amene wakhala mʼbusa wanga moyo wanga wonse mpaka lero,+
16 Mngelo amene wakhala akundiwombola ku masoka anga onse,+ adalitse anyamatawa.+
Anawa azidziwika ndi dzina langa komanso mayina a makolo anga, Abulahamu ndi Isaki,
Anawa adzachulukane nʼkukhala gulu la anthu ambiri padziko lapansi.”+
-