Machitidwe 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mose anabadwa pa nthawi imeneyi, ndipo Mulungu ankamuona kuti ndi wokongola. Iye analeredwa mʼnyumba ya bambo ake kwa miyezi itatu.+
20 Mose anabadwa pa nthawi imeneyi, ndipo Mulungu ankamuona kuti ndi wokongola. Iye analeredwa mʼnyumba ya bambo ake kwa miyezi itatu.+