Yoswa 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mzindawu komanso zinthu zonse zimene zilimo ziyenera kuwonongedwa,+ zonse ndi za Yehova. Rahabi+ yekha, hule uja, musamuphe. Mumusiye pamodzi ndi onse amene ali nawo mʼnyumba mwake, chifukwa iye anabisa anthu amene tinawatuma.+
17 Mzindawu komanso zinthu zonse zimene zilimo ziyenera kuwonongedwa,+ zonse ndi za Yehova. Rahabi+ yekha, hule uja, musamuphe. Mumusiye pamodzi ndi onse amene ali nawo mʼnyumba mwake, chifukwa iye anabisa anthu amene tinawatuma.+