Oweruza 13:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Patapita nthawi, mkaziyo anabereka mwana wamwamuna ndipo anamupatsa dzina lakuti Samisoni.+ Pamene mnyamatayo ankakula, Yehova anapitiriza kumudalitsa.
24 Patapita nthawi, mkaziyo anabereka mwana wamwamuna ndipo anamupatsa dzina lakuti Samisoni.+ Pamene mnyamatayo ankakula, Yehova anapitiriza kumudalitsa.